Lyrics
Artist: BLEZEL
Beib, kodi ukazanditalikira... kirah,
Zaine uzakhala ukukumbukira!
Kodi beib, ungandipatse chitsimikizo chotani?
Kuti mtima wanga, za iwe, uzizawerenga.
Coz ndizizati ndikafatsa-fatsa,
Ndiziganiza ukuyenda ndi wina,
Muli kuchitanso mwina zina.
Beib, chomwe ndikufuna
Ndi chitsimikizo,
Kuti mtima wanga
Usamazadandaulenso.
Pano ndikufuna chitsimikizo,
(Simikizo) ×2.
Beib, you know that I love you more,
And I want to be with you.
So now ndingofuna chitsimikizo,
(Simikizo) ×2.
Simikiza, beib!
Kulikonse komwe ungayende-yende,
Chilichonse chomwe ungachite,
Kodi za ine uzakhala ukuwerengera?
Mtima wazaza ndi mafunso,
Ndipo ukufuna chitsimikizo.
Beib, nditsimikizile pondikumbatira,
For sure, ndimafuna mtazakukwatira.
Ndipo suzalira,
Ine ndidzakusamalira.
Koma pano ungonditsimikizira,
Kuti ukazanditalikira,
Suzanditalikira... aaaah!
This song was made with StarSinger
Describe a person or a moment in a few words. StarSinger writes the lyrics and sings it.
FAQ
Who made "CHITSIMIKIZO"?
"CHITSIMIKIZO" was made by @endless_magpie_55 on Star Singer, where anyone can write and sing an original song with AI.
What genre is CHITSIMIKIZO?
CHITSIMIKIZO is Pop.
Can I listen to "CHITSIMIKIZO" for free?
Yes. "CHITSIMIKIZO" streams free on Star Singer — no subscription required. You can also make your own: one AI song a day is free, extra songs with a lyric video are $1.99, a lip-synced music video starring you is $19.99, and cinematic videos start at $2.99.
Can I create my own AI song?
Yes. Star Singer lets you create AI-generated songs and music videos. Clone your voice, pick any style, and generate original music. Listening is free and unlimited, and one song a day is free to make — no subscription.
Thanks — this has been sent to our review team.